Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 136:26 - Buku Lopatulika

26 Yamikani Mulungu wa Kumwamba, pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Yamikani Mulungu wa kumwamba; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Thokozani Mulungu wakumwamba, pakuti chikondi chake nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Yamikani Mulungu wakumwamba, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 136:26
8 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali, pakumva mau awa, ndinakhala pansi ndi kulira misozi, ndi kuchita maliro masiku ena, ndinasalanso, ndi kupemphera pamaso pa Mulungu wa Kumwamba,


Ndipo mfumu inati kwa ine, Ufunanji iwe? Pamenepo ndinapemphera Mulungu wa Kumwamba.


Koma Mulungu wathu ndiye ali m'mwamba; achita chilichonse chimkonda.


Ndikweza maso anga kwa Inu, kwa Inu wakukhala kumwamba.


kuti apemphe zachifundo kwa Mulungu wa Kumwamba pa chinsinsi ichi; kuti Daniele ndi anzake asaonongeke pamodzi ndi eni nzeru ena a ku Babiloni.


Ndipo ananena nao, Ndine Muhebri, ndiopa Yehova Mulungu wa Kumwamba, amene analenga nyanja ndi mtunda.


Ndipo panthawipo panali chivomezi chachikulu, ndipo limodzi la magawo khumi a mzinda lidagwa; ndipo anaphedwa m'chivomezicho anthu zikwi zisanu ndi ziwiri; ndipo otsalawo anakhala amantha, napatsa ulemerero kwa Mulungu wa mu Mwamba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa