Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 136:25 - Buku Lopatulika

25 Ndiye wakupatsa nyama zonse chakudya; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndiye wakupatsa nyama zonse chakudya; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Amapatsa zamoyo zonse chakudya, pakuti chikondi chake nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Amene amapereka chakudya kwa cholengedwa chilichonse, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 136:25
4 Mawu Ofanana  

Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, nudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.


Izi zonse zikulindirirani, muzipatse chakudya chao pa nyengo yake.


Maso a onse ayembekeza Inu; ndipo muwapatsa chakudya chao m'nyengo zao.


Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa