Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 136:20 - Buku Lopatulika

20 Ndi Ogi mfumu ya Basani; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndi Ogi mfumu ya Basani; pakuti chifundo chake nchosatha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Adapha Ogi, mfumu ya ku Basani, pakuti chikondi chake nchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Ogi mfumu ya Basani, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 136:20
2 Mawu Ofanana  

Ndipo anatembenuka nakwera kudzera njira ya ku Basani; ndipo Ogi mfumu ya ku Basani anatuluka kukumana nao, iye ndi anthu ake onse, kudzachita nao nkhondo ku Ederei.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa