Masalimo 130:6 - Buku Lopatulika6 Moyo wanga uyang'anira Ambuye, koposa alonda matanda kucha; inde koposa alonda matanda kucha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Moyo wanga uyang'anira Ambuye, koposa alonda matanda kucha; inde koposa alonda matanda kucha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mtima wanga umayembekeza Chauta kupambana m'mene alonda amayembekezera mbandakucha, kupambanadi m'mene alonda amayembekezera mbandakucha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Moyo wanga umayembekezera Ambuye, kupambana momwe alonda amayembekezera mmawa, inde, kupambana momwe alonda amayembekezera mmawa, Onani mutuwo |