Masalimo 129:8 - Buku Lopatulika8 Angakhale opitirirapo sanena, Dalitso la Mulungu likhale pa inu; tikudalitsani m'dzina la Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Angakhale opitirirapo sanena, Dalitso la Mulungu likhale pa inu; tikudalitsani m'dzina la Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Anthu odutsapo sadzanena kwa omwetawo kuti, “Madalitso a Chauta akhale nanu.” “Tikukudalitsani potchula dzina la Chauta.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Odutsa pafupi asanene kuti, “Dalitso la Yehova lili pa inu; tikukudalitsani mʼdzina la Yehova.” Onani mutuwo |