Masalimo 129:7 - Buku Lopatulika7 umene womweta sadzaza nao dzanja lake, kapena womanga mitolo sakupatira manja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 umene womweta sadzaza nao dzanja lake, kapena womanga mitolo sakupatira manja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Woumweta sangadzaze nkumanja komwe, womanga mitolo sangamange nchitsakato chomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 sungadzaze manja a owumweta kapena manja a omanga mitolo. Onani mutuwo |