Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 125:4 - Buku Lopatulika

4 Chitirani chokoma, Yehova, iwo okhala okoma; iwo okhala oongoka mumtima mwao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Chitirani chokoma, Yehova, iwo okhala okoma; iwo okhala oongoka mumtima mwao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Chauta, achitireni zabwino anthu amene ali abwino, amene ali olungama mtima.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Yehova chitirani zabwino amene ndi abwino, amene ndi olungama mtima

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 125:4
17 Mawu Ofanana  

Inu ndinu wabwino, ndi wakuchita zabwino; mundiphunzitse malemba anu.


Mtima wanga ukhale wangwiro m'malemba anu; kuti ndisachite manyazi.


Wodala munthuyu Yehova samwerengera mphulupulu zake; ndimo mumzimu mwake mulibe chinyengo.


Tanimphitsani chifundo chanu pa iwo akudziwa Inu; ndi chilungamo chanu pa oongoka mtima.


Chitirani Ziyoni chokoma monga mwa kukondwera kwanu; mumange malinga a miyala a Yerusalemu.


Chikopa changa chili ndi Mulungu, wopulumutsa oongoka mtima.


Indedi Mulungu achitira Israele zabwino, iwo a mtima wa mbee.


Pakuti Yehova Mulungu ndiye dzuwa ndi chikopa; Yehova adzapatsa chifundo ndi ulemerero; sadzakaniza chokoma iwo akuyenda angwiro.


Yehova wa makamu, wodala munthu wakukhulupirira Inu.


Pakuti chiweruzo chidzabwera kunka kuchilungamo, ndipo oongoka mtima onse adzachitsata.


Yehova akhalira wabwino omlindirira, ndi moyo womfunafuna.


Yesu anaona Natanaele alinkudza kwa Iye, nanena za iye, Onani, Mwisraele ndithu, mwa iye mulibe chinyengo!


pakuti Mulungu sali wosalungama kuti adzaiwala ntchito yanu, ndi chikondicho mudachionetsera kudzina lake, umo mudatumikira oyera mtima ndi kuwatumikirabe.


Ndipo m'kamwa mwao simunapezedwe bodza; ali opanda chilema.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa