Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 124:8 - Buku Lopatulika

8 Thandizo lathu lili m'dzina la Yehova, wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Thandizo lathu lili m'dzina la Yehova, wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Chithandizo chathu chimachokera kwa Chauta, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Thandizo lathu lili mʼdzina la Yehova wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 124:8
10 Mawu Ofanana  

Pachiyambi Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Inu ndinu Yehova, nokhanu; mwalenga thambo, kumwambamwamba, ndi khamu lao lonse, dziko lapansi, ndi zonse zili pomwepo, nyanja ndi zonse zili m'mwemo, ndi Inu muzisunga zamoyo zonsezi, ndi khamu lakumwamba lilambira Inu.


Odalitsika inu a kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Thandizo langa lidzera kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Yehova, ali mu Ziyoni, akudalitseni; ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Iwowa anagonjeka, nagwa; koma ife tauka, ndipo takhala chilili.


Ha! Yehova Mulungu, taonani, Inu munalenga kumwamba ndi dziko lapansi ndi mphamvu yanu yaikulu ndi mkono wanu wotambasuka; palibe chokanika Inu;


Ndipo m'mene adamva, anakweza mau kwa Mulungu ndi mtima umodzi, nati, Mfumu, Inu ndinu wolenga thambo la kumwamba ndi dziko, ndi nyanja, ndi zonse zili m'menemo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa