Masalimo 124:6 - Buku Lopatulika6 Alemekezedwe Yehova, amene sanatipereke kumano kwao tikhale chakudya chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Alemekezedwe Yehova, amene sanatipereke kumano kwao tikhale chakudya chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Atamandike Chauta, amene sadatipereke kwa anthuwo kuti atiwononge. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Atamandike Yehova, amene sanalole kuti tikhale chakudya cha mano awo. Onani mutuwo |