Masalimo 119:93 - Buku Lopatulika93 Sindidzaiwala malangizo anu nthawi zonse; popeza munandipatsa nao moyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201493 Sindidzaiwala malangizo anu nthawi zonse; popeza munandipatsa nao moyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa93 Sindidzaiŵala konse malangizo anu, pakuti mwandipatsa nawo moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero93 Ine sindidzayiwala konse malangizo anu, pakuti ndi malangizo anuwo munasunga moyo wanga. Onani mutuwo |