Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:92 - Buku Lopatulika

92 Chilamulo chanu chikadapanda kukhala chikondweretso changa, ndikadatayika m'kuzunzika kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

92 Chilamulo chanu chikadapanda kukhala chikondweretso changa, ndikadatayika m'kuzunzika kwanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

92 Malamulo anu akadapanda kundisangalatsa, bwenzi nditafa ndi mazunzo anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

92 Malamulo anu akanapanda kukhala chikondwerero changa, ndikanawonongeka mʼmasautso anga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:92
9 Mawu Ofanana  

Kusautsika ndi kupsinjika kwandigwera; koma malamulo anu ndiwo ondikondweretsa ine.


Ndidzadzikondweretsa nao malemba anu; sindidzaiwala mau anu.


Mboni zanu zomwe ndizo zondikondweretsa, ndizo zondipangira nzeru.


Chitonthozo changa m'kuzunzika kwanga ndi ichi; pakuti mau anu anandipatsa moyo.


Nsoni zokoma zanu zindidzere, kuti ndikhale ndi moyo; popeza chilamulo chanu chindikondweretsa.


Ndikadapanda kukhulupirira kuti ndikaone ubwino wa Yehova m'dziko la amoyo, ndikadatani!


Pakuti zonse zinalembedwa kale zinalembedwa kutilangiza, kuti mwa chipiriro ndi chitonthozo cha malembo, tikhale ndi chiyembekezo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa