Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:91 - Buku Lopatulika

91 Kunena za maweruzo anu alimbikira kufikira lero; pakuti onsewa ndiwo atumiki anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

91 Kunena za maweruzo anu alimbikira kufikira lero; pakuti onsewa ndiwo atumiki anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

91 Zolengedwa zikupezeka lero lino chifukwa cha kulamula kwanu, pakuti zinthu zonse zimakutumikirani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

91 Malamulo anu alipobe mpaka lero lino, pakuti zinthu zonse zimatumikira Inu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:91
10 Mawu Ofanana  

Pakukhalabe masiku a dziko lapansi, nthawi yakubzala ndi yakukunkha, chisanu ndi mafundi, malimwe ndi msakasa, usana ndi usiku sizidzalekai.


Kwezani maso anu kumwamba, muone amene analenga izo, amene atulutsa khamu lao ndi kuziwerenga; azitcha zonse maina ao, ndi mphamvu zake zazikulu, ndi popeza ali wolimba mphamvu, palibe imodzi isoweka.


Inde dzanja langa linakhazika maziko a dziko lapansi, ndi dzanja langa lamanja linafunyulula m'mwamba; pakuziitana Ine ziimirira pamodzi.


Yehova atero: Likaleka kukhala pangano langa la usana ndi usiku, ngati sindinalemba malemba a kumwamba ndi dziko lapansi;


kotero kuti mukakhale ana a Atate wanu wa Kumwamba; chifukwa Iye amakwezera dzuwa lake pa oipa ndi pa abwino, namavumbitsira mvula pa olungama ndi pa osalungama.


Pakuti inenso ndili munthu wakumvera ulamuliro, ndili nao asilikali akundimvera ine: ndipo ndinena kwa uyu, Muka, namuka; ndi kwa wina, Idza, nadza; ndi kwa kapolo wanga, Chita ichi, nachita.


ndi kuti mungakweze maso anu kupenya kumwamba, ndipo poona dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi, khamu lonse la kumwamba, munganyengedwe ndi kuzigwadira, ndi kuzitumikira, zimene Yehova Mulungu wanu anagawira mitundu yonse ya anthu pansi pa thambo lonse.


Nyenyezi zinathira nkhondo yochokera kumwamba, m'mipita mwao zinathirana ndi Sisera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa