Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:88 - Buku Lopatulika

88 Mundipatse moyo monga mwa chifundo chanu; ndipo ndidzasamalira mboni ya pakamwa panu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

88 Mundipatse moyo monga mwa chifundo chanu; ndipo ndidzasamalira mboni ya pakamwa panu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

88 Sungani moyo wanga chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika, kuti nditsate malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

88 Sungani moyo wanga molingana ndi chikondi chanu chosasinthika, ndipo ndidzamvera umboni wa pakamwa panu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:88
10 Mawu Ofanana  

Muchitire mtumiki wanu monga mwa chifundo chanu, ndipo ndiphunzitseni malemba anu.


Ndinaitanira Inu; ndipulumutseni, ndipo ndidzasamalira mboni zanu.


Imvani liu langa monga mwa chifundo chanu; mundipatse moyo monga mwa kuweruza kwanu, Yehova.


Penyani kuti ndikonda malangizo anu; mundipatse moyo, Yehova, monga mwa chifundo chanu.


Odala iwo akusunga mboni zake, akumfuna ndi mtima wonse;


Moyo wanga umamatika ndi fumbi; mundipatse moyo monga mwa mau anu.


Taonani, ndinalira malangizo anu; mundipatse moyo mwa chilungamo chanu.


Ana ako akasunga chipangano changa ndi mboni yanga imene ndidzawaphunzitsa, ana aonso adzakhala pa mpando wanu kunthawi zonse,


Mayendedwe onse a Yehova ndiwo chifundo ndi choonadi, kwa iwo akusunga pangano lake ndi mboni zake.


Anakhazika mboni mwa Yakobo, naika chilamulo mwa Israele, ndizo analamulira atate athu, akazidziwitse ana ao;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa