Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:85 - Buku Lopatulika

85 Odzikuza anandikumbira mbuna, ndiwo osasamalira chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

85 Odzikuza anandikumbira mbuna, ndiwo osasamalira chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

85 Anthu osasamala za Mulungu, osatsata malamulo anu, andikumbira mbuna.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

85 Anthu osalabadira za Mulungu, odzikuza amandikumbira dzenje motsutsana ndi malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:85
8 Mawu Ofanana  

Odzikuza achite manyazi, popeza anandichitira monyenga ndi bodza: Koma ine ndidzalingalira malangizo anu.


Pakuti ananditchera ukonde wao m'mbunamo kopanda chifukwa, anakumbira moyo wanga dzenje kopanda chifukwa.


Phazi la akudzikuza lisandifikire ine, ndi dzanja la oipa lisandichotse.


Anachita dzenje, nalikumba, nagwa m'mbuna yomwe anaikumba.


Munthu wopanda pake akonzeratu zoipa; ndipo m'milomo mwake muli moto wopsereza.


Kodi choipa chibwezedwe pa chabwino? Pakuti akumbira moyo wanga dzenje. Mukumbukire kuti ndinaima pamaso panu kuwanenera zabwino, kuwachotsera iwo ukali wanu.


Mfuu umvekedwe m'nyumba zao, pamene muwatengera khamu la nkhondo dzidzidzi; pakuti akumba dzenje lakundigwira ine, anabisira mapazi anga misampha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa