Masalimo 119:83 - Buku Lopatulika83 Popeza ndakhala ngati thumba lofukirira; koma sindiiwala malemba anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201483 Popeza ndakhala ngati thumba lofukirira; koma sindiiwala malemba anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa83 Ndasanduka ngati thumba lachikopa lokhwinyata, komabe sindiiŵala malamulo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero83 Ngakhale ndili ngati thumba lachikopa la vinyo pa utsi sindiyiwala zophunzitsa zanu. Onani mutuwo |