Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:81 - Buku Lopatulika

81 Moyo wanga unakomoka ndi kukhumba chipulumutso chanu: Ndinayembekezera mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

81 Moyo wanga unakomoka ndi kukhumba chipulumutso chanu: Ndinayembekezera mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

81 Moyo wanga wafooka podikira chipulumutso chanu, ndikukhulupirira mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

81 Moyo wanga wafowoka ndi kufunafuna chipulumutso chanu, koma chiyembekezo changa chili mʼmawu anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:81
15 Mawu Ofanana  

amene ndidzampenya ndekha, ndi maso anga adzamuona, si wina ai. Imso zanga zatha m'kati mwanga.


Inu ndinu pobisalapo panga, ndi chikopa changa; ndiyembekezera mau anu.


Mtima wanga wasweka ndi kukhumba maweruzo anu nyengo zonse.


Taonani, ndinalira malangizo anu; mundipatse moyo mwa chilungamo chanu.


Ndipo chifundo chanu chindidzere, Yehova, ndi chipulumutso chanu, monga mwa mau anu.


Kuti ndikhale nao mau akuyankha wonditonza; popeza ndikhulupirira mau anu.


Ndipo musandichotsere ndithu mau a choonadi pakamwa panga; pakuti ndinayembekeza maweruzo anu.


Iwo amene akuopani adzandiona ine nadzakondwera; popeza ndayembekezera mau anu.


Nsoni zokoma zanu zindidzere, kuti ndikhale ndi moyo; popeza chilamulo chanu chindikondweretsa.


Ndilindira Yehova, moyo wanga ulindira, ndiyembekeza mau ake.


Likatha thupi langa ndi mtima wanga, Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga, ndi cholandira changa chosatha.


Moyo wanga ulakalaka, inde ukomokanso ndi kufuna mabwalo a Yehova; mtima wanga ndi thupi langa zifuulira kwa Mulungu wamoyo.


Ndikulumbirirani, ana aakazi inu a ku Yerusalemu, mukapeza bwenzi langa, mudzamuuza chiyani? Kuti ndadwala ndi chikondi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa