Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:80 - Buku Lopatulika

80 Mtima wanga ukhale wangwiro m'malemba anu; kuti ndisachite manyazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

80 Mtima wanga ukhale wangwiro m'malemba anu; kuti ndisachite manyazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

80 Mtima wanga ukhale wopanda choudzudzulira pa malamulo anu, kuti ndisachite manyazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

80 Mtima wanga ukhale wopanda cholakwa pa chiphunzitso chanu kuti ndisachititsidwe manyazi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:80
14 Mawu Ofanana  

Koma anachita choipa, popeza sanalunjikitse mtima wake kufuna Yehova.


Chinkana misanje siinachotsedwe mu Israele, mtima wa Asa unali wangwiro masiku ake onse.


Ndipo anachita zoongoka pamaso pa Yehova, koma wosachita ndi mtima wangwiro.


Pamenepo sindidzachita manyazi, pakupenyerera malamulo anu onse.


Ungwiro ndi kuongoka mtima zindisunge, pakuti ndayembekezera Inu.


Wodala munthuyu Yehova samwerengera mphulupulu zake; ndimo mumzimu mwake mulibe chinyengo.


Chinjiriza mtima wako koposa zonse uzisunga; pakuti magwero a moyo atulukamo.


Ndipo ndidzakutulutsani m'kati mwake, ndi kukuperekani m'manja a alendo, ndi kuchita maweruzo pakati panu.


Yesu anaona Natanaele alinkudza kwa Iye, nanena za iye, Onani, Mwisraele ndithu, mwa iye mulibe chinyengo!


Pakuti kudzitamandira kwathu ndiko umboni wa chikumbumtima chathu, kuti m'chiyero ndi kuona mtima kwa Mulungu, si m'nzeru ya thupi, koma m'chisomo cha Mulungu tinadzisunga m'dziko lapansi, koma koposa kwa inu.


Lero lino Yehova Mulungu wanu akulamulirani kuchita malemba ndi maweruzo awa; potero muzimvera ndi kuwachita ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse.


Ndipo tsopano, tiana, khalani mwa Iye; kuti akaonekere Iye tikakhale nako kulimbika mtima, osachita manyazi kwa Iye pa kudza kwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa