Masalimo 119:74 - Buku Lopatulika74 Iwo amene akuopani adzandiona ine nadzakondwera; popeza ndayembekezera mau anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201474 Iwo amene akuopani adzandiona ine nadzakondwera; popeza ndayembekezera mau anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa74 Anthu okuwopani adzandiwona ndipo adzakondwa, popeza kuti ndakhulupirira mau anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero74 Iwo amene amakuopani akondwere akandiona, chifukwa chiyembekezo changa chili mʼmawu anu. Onani mutuwo |