Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:72 - Buku Lopatulika

72 Chilamulo cha pakamwa panu chindikomera koposa golide ndi siliva zikwizikwi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

72 Chilamulo cha pakamwa panu chindikomera koposa golide ndi siliva zikwizikwi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

72 Malamulo a pakamwa panu amandikomera kuposa ndalama zikwizikwi zagolide ndi zasiliva.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

72 Lamulo lochokera mʼkamwa mwanu limandikomera kwambiri kuposa ndalama zambirimbiri za siliva ndi golide.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:72
13 Mawu Ofanana  

Ndinalandira mboni zanu zikhale cholandira chosatha; pakuti ndizo zokondweretsa mtima wanga.


Chifukwa chake ndikonda malamulo anu koposa golide, inde golide woyengeka.


Ndinakondwera m'njira ya mboni zanu, koposa ndi chuma chonse.


Ndikondwera nao mau anu, ngati munthu wakupeza zofunkha zambiri.


Ndizo zifunika koposa golide, inde, golide wambiri woyengetsa; zizuna koposa uchi ndi zakukha za zisa zake.


Ndiponso kapolo wanu achenjezedwa nazo, m'kuzisunga izo muli mphotho yaikulu.


Kodi kulandira nzeru sikupambana ndi golide, kulandira luntha ndi kusankhika koposa siliva?


Wodala ndi wopeza nzeru, ndi woona luntha;


Chipatso changa chiposa golide, ngakhale golide woyengeka; phindu langa liposa siliva wosankhika.


Nzeru ili yabwino pamodzi ndi cholowa; akuona dzuwa apindula nayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa