Masalimo 119:71 - Buku Lopatulika71 Kundikomera kuti ndinazunzidwa; kuti ndiphunzire malemba anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201471 Kundikomera kuti ndinazunzidwa; kuti ndiphunzire malemba anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa71 Ndi bwino kuti ndidalangidwa, kuti ndiphunzire malamulo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero71 Ndi bwino kuti ndinasautsidwa kuti ndithe kuphunzira malamulo anu. Onani mutuwo |