Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:70 - Buku Lopatulika

70 Mtima wao unona ngati mafuta; koma ine ndikondwera nacho chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

70 Mtima wao unona ngati mafuta; koma ine ndikondwera nacho chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

70 Anthu otere ndi opulukira, koma ine ndimakondwa ndi malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

70 Mitima yawo ndi yowuma ndi yosakhudzidwa, koma ine ndimakondwera ndi malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:70
8 Mawu Ofanana  

Ndidzadzikondweretsa nao malemba anu; sindidzaiwala mau anu.


Mundiyendetse mopita malamulo anu; pakuti ndikondwera m'menemo.


Mafuta ao awatsekereza; m'kamwa mwao alankhula modzikuza.


kuchita chikondwero chanu kundikonda, Mulungu wanga; ndipo malamulo anu ali m'kati mwamtima mwanga.


Kunenepa kwao kutuzulitsa maso ao, malingaliro a mitima yao asefukira.


Nenepetsa mtima wa anthu awa, lemeretsa makutu ao, nutseke maso ao; angaone ndi maso ao, angamve ndi makutu ao, angazindikire ndi mtima wao, nakabwerenso, nachiritsidwe.


pakuti mtima wa anthu awa watupatu, ndipo m'makutu mwao mmolema kumva, ndipo maso ao anawatseka; kuti angaone ndi maso, nangamve ndi makutu, nangazindikire ndi mtima, nangatembenuke, ndipo Ine ndingawachiritse.


Pakuti monga mwa munthu wa m'kati mwanga, ine ndikondwera ndi chilamulo cha Mulungu:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa