Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:61 - Buku Lopatulika

61 Anandikulunga nazo zingwe za oipa; koma sindinaiwale chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

61 Anandikulunga nazo zingwe za oipa; koma sindinaiwala chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

61 Ngakhale anthu oipa anditchere msampha, sindiiŵala malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

61 Ngakhale oyipa andimange ndi zingwe, sindidzayiwala lamulo lanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:61
12 Mawu Ofanana  

Akali chilankhulire uyu, anadza winanso, nati, Ababiloni anadzigawa magulu atatu, nazigwera ngamira, nazitenga, nawapha anyamata ndi lupanga lakuthwa, ndipo ndapulumuka ine ndekha kudzakuuzani.


Ndidzadzikondweretsa nao malemba anu; sindidzaiwala mau anu.


Ndinasochera ngati nkhosa yotayika; funani mtumiki wanu; pakuti sindiiwala malamulo anu.


Oipa anandilalira kundiononga; koma ndizindikira mboni zanu.


Odzikuza ananditchera msampha, nandibisira zingwe; anatcha ukonde m'mphepete mwa njira; ananditchera makwekwe.


Yehova! Ha! Achuluka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri.


Usanene, Ndidzamchitira zomwezo anandichitira ine ndidzabwereza munthuyo monga mwa machitidwe ake.


Ndipo monga magulu a mbala alalira munthu, momwemo msonkhano wa ansembe amapha panjira ya ku Sekemu; indedi achita choipitsitsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa