Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:54 - Buku Lopatulika

54 Malemba anu anakhala nyimbo zanga m'nyumba ya ulendo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

54 Malemba anu anakhala nyimbo zanga m'nyumba ya ulendo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

54 Malamulo anu asanduka nyimbo yanga kulikonse kumene ndimapita.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

54 Zophunzitsa zanu ndi mitu ya nyimbo yanga kulikonse kumene ndigonako.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:54
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yakobo anati kwa Farao, Masiku a zaka za ulendo wanga ndi zaka zana limodzi kudza makumi atatu; masiku a zaka za moyo wanga ali owerengeka ndi oipa, sanafikire masiku a zaka za moyo wa makolo anga m'masiku a ulendo wao.


Muimiranji patali, Yehova? Mubisaliranji m'nyengo za nsautso?


Ndidzaimbira zachifundo za Yehova nthawi yonse, pakamwa panga ndidzadziwitsira chikhulupiriko chanu ku mibadwomibadwo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa