Masalimo 119:52 - Buku Lopatulika52 Ndinakumbukira maweruzo anu kuyambira kale, Yehova, ndipo ndinadzitonthoza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Ndinakumbukira maweruzo anu kuyambira kale, Yehova, ndipo ndinadzitonthoza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Inu Chauta, ndikamalingalira malamulo anu akalekale, ndimasangalala, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Ndimakumbukira malamulo anu Yehova akalekale, ndipo mwa iwo ndimapeza chitonthozo. Onani mutuwo |