Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:51 - Buku Lopatulika

51 Odzikuza anandinyoza kwambiri: koma sindinapatukanso nacho chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

51 Odzikuza anandinyoza kwambiri: koma sindinapatukanso nacho chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

51 Anthu osasamala za Mulungu amandinyoza kwathunthu, komabe sindisiyana nawo malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

51 Odzikuza amandinyoza popanda chowaletsa, koma sindichoka pa malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:51
14 Mawu Ofanana  

Phazi langa lagwiratu moponda Iye, ndasunga njira yake, wosapatukamo.


Ondilondola ndi ondisautsa ndiwo ambiri; koma sindinapatukane nazo mboni zanu.


Munadzudzula odzikuza otembereredwa, iwo akusokera kusiyana nao malamulo anu.


Ndimamatika nazo mboni zanu; musandichititse manyazi, Yehova.


Odzikuza anandipangira bodza: Ndidzasunga malangizo anu ndi mtima wanga wonse.


Mtima wathu sunabwerere m'mbuyo, ndipo m'mayendedwe athu sitinapatuke m'njira yanu;


Kumbukiranitu tsopano, Yehova, kuti ndayenda pamaso panu m'zoonadi ndi mtima wangwiro, ndipo ndachita zabwino pamaso panu. Ndipo Hezekiya analira kolimba.


Iye sadzalephera kapena kudololoka, kufikira atakhazikitsa chiweruzo m'dziko lapansi; ndipo zisumbu zidzalindira chilamulo chake.


Yehova, mwandikopa ine, ndipo ndinakopedwa; muli ndi mphamvu koposa ine, ndipo mwapambana; ine ndikhala choseketsa dzuwa lonse, onse andiseka.


Ndipo anthu anaima alikupenya. Ndi akulunso anamlalatira Iye, nanena, Anapulumutsa ena; adzipulumutse yekha ngati iye ndiye Khristu wa Mulungu, wosankhidwa wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa