Masalimo 119:44 - Buku Lopatulika44 Potero ndidzasamalira malamulo anu chisamalire kunthawi za nthawi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Potero ndidzasamalira malamulo anu chisamalire kunthawi za nthawi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Ndidzatsata malamulo anu kosalekeza mpaka muyaya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Ndidzasunga malamulo anu nthawi zonse, ku nthawi za nthawi. Onani mutuwo |