Masalimo 119:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo musandichotsere ndithu mau a choonadi pakamwa panga; pakuti ndinayembekeza maweruzo anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo musandichotsere ndithu mau a choonadi pakamwa panga; pakuti ndinayembekeza maweruzo anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Pakamwa panga musapaletse mpang'ono pomwe kulankhula mau anu oona, pakuti ndimakhulupirira malangizo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Musakwatule mawu a choonadi mʼkamwa mwanga, pakuti ndakhazikitsa chiyembekezo changa mʼmalamulo anu. Onani mutuwo |