Masalimo 119:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo chifundo chanu chindidzere, Yehova, ndi chipulumutso chanu, monga mwa mau anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo chifundo chanu chindidzere, Yehova, ndi chipulumutso chanu, monga mwa mau anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Chauta, mundikonde ndi chikondi chanu chosasinthika, mundipulumutse monga momwe mudalonjezera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Chikondi chanu chosasinthika chibwere kwa ine, Inu Yehova, chipulumutso chanu monga mwa lonjezo lanu; Onani mutuwo |