Masalimo 119:23 - Buku Lopatulika23 Nduna zomwe zinakhala zondineneza; koma mtumiki wanu analingirira malemba anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Nduna zomwe zinakhala zondineneza; koma mtumiki wanu analingirira malemba anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ngakhale mafumu andichitire upo woipa, ine mtumiki wanu ndidzasinkhasinkhabe za malamulo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ngakhale mafumu akhale pamodzi kundinyoza, mtumiki wanu adzalingalirabe zophunzitsa zanu. Onani mutuwo |