Masalimo 119:22 - Buku Lopatulika22 Mundichotsere chotonza, ndi chimpepulo; pakuti ndinasunga mboni zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Mundichotsere chotonza, ndi chimpepulo; pakuti ndinasunga mboni zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Mundichotsere zonyoza zao zondinyodola, chifukwa ndasunga malamulo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Mundichotsere chitonzo ndi mnyozo pakuti ndimasunga malamulo anu. Onani mutuwo |
Ndipo pamene Davide anamva kuti Nabala adamwalira, iye anati, Alemekezedwe Yehova, amene anaweruza mlandu wa mtonzo wanga wochokera ku dzanja la Nabala, naletsa mnyamata wake pa choipa; ndipo Yehova anabwezera pamutu pa Nabala choipa chake. Ndipo Davide anatumiza wokamfunsira Abigaile, zakuti amtengere akhale mkazi wake.