Masalimo 119:166 - Buku Lopatulika166 Ndinayembekeza chipulumutso chanu, Yehova, ndipo ndinachita malamulo anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 2014166 Ndinayembekeza chipulumutso chanu, Yehova, ndipo ndinachita malamulo anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa166 Ndimakhulupirira kuti mudzandipulumutsa, Inu Chauta, ndipo ndimatsata malamulo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero166 Ndikudikira chipulumutso chanu, Inu Yehova, ndipo ndimatsatira malamulo anu. Onani mutuwo |