Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:162 - Buku Lopatulika

162 Ndikondwera nao mau anu, ngati munthu wakupeza zofunkha zambiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

162 Ndikondwera nao mau anu, ngati munthu wakupeza zofunkha zambiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

162 Ndimakondwa ndi mau anu monga munthu amene wapeza chuma chambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

162 Ine ndimakondwa ndi lonjezo lanu, ngati munthu amene wapeza chuma chambiri.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:162
7 Mawu Ofanana  

Ndinalandira mboni zanu zikhale cholandira chosatha; pakuti ndizo zokondweretsa mtima wanga.


Ndinakondwera m'njira ya mboni zanu, koposa ndi chuma chonse.


Chilamulo cha pakamwa panu chindikomera koposa golide ndi siliva zikwizikwi.


Kufatsa mtima ndi osauka kuposa kugawana zofunkha ndi onyada.


Inu mwachulukitsa mtundu, inu mwaenjezera kukondwa kwao; iwo akondwa pamaso panu monga akondwera m'masika, monga anthu akondwa pogawana zofunkha.


Mau anu anapezeka, ndipo ndinawadya; mau anu anakhala kwa ine chikondwero ndi chisangalalo cha mtima wanga; pakuti ndatchedwa dzina lanu, Yehova Mulungu wa makamu.


Ndipo pamene anatsika naye, onani, iwo anabalalika apo ponse, analinkudya, ndi kumwa, ndi kudyerera, chifukwa cha chofunkha zambiri anazitenga ku dziko la Afilisti, ndi ku dziko la Yuda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa