Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:155 - Buku Lopatulika

155 Chipulumutso chitalikira oipa; popeza safuna malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

155 Chipulumutso chitalikira oipa; popeza safuna malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

155 Chipulumutso chili kutali ndi anthu oipa, pakuti safunafuna malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

155 Chipulumutso chili kutali ndi anthu oyipa, pakuti iwowo safunafuna zophunzitsa zanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:155
11 Mawu Ofanana  

Ana ake akhala otekeseka, napsinjika kuchipata, wopanda wina wakuwapulumutsa.


Woipa, monga mwa kudzikuza kwa nkhope yake, akuti, Sadzafunsira. Malingaliro ake onse akuti, Palibe Mulungu.


Pakuti Inu muwapulumutsa anthu aumphawi; koma maso okweza muwatsitsa.


Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha kudziwa; opusa anyoza nzeru ndi mwambo.


Mverani Ine, inu olimba mtima, amene muli kutali ndi chilungamo;


Ndilenga chipatso cha milomo, Mtendere, mtendere kwa iye amene ali kutali, ndi kwa iye amene ali chifupi, ati Yehova; ndipo ndidzamchiritsa iye.


Tonse tibangula ngati zilombo, ndi kulira maliro zolimba ngati nkhunda; tiyang'anira chiweruziro koma palibe; tiyang'anira chipulumutso koma chili patali ndi ife.


Ndipo anakweza mau nati, Atate Abrahamu, mundichitire chifundo, mutume Lazaro, kuti aviike nsonga ya chala chake m'madzi, naziziritse lilime langa; pakuti ndizunzidwadi m'lawi ili la moto.


palibe mmodzi wakudziwitsa, palibe mmodzi wakulondola Mulungu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa