Masalimo 119:146 - Buku Lopatulika146 Ndinaitanira Inu; ndipulumutseni, ndipo ndidzasamalira mboni zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 2014146 Ndinaitanira Inu; ndipulumutseni, ndipo ndidzasamalira mboni zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa146 Ndikukulirirani, mundipulumutse, kuti ndizitsata malamulo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero146 Ndikuyitana kwa Inu; pulumutseni ndipo ndidzasunga umboni wanu. Onani mutuwo |