Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:145 - Buku Lopatulika

145 Ndinaitana ndi mtima wanga wonse; mundiyankhe, Yehova; ndidzasunga malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

145 Ndinaitana ndi mtima wanga wonse; mundiyankhe, Yehova; ndidzasunga malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

145 Ndikulira kwa Inu ndi mtima wanga wonse, mundiyankhe, Inu Chauta. Ndidzatsata malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

145 Ndimayitana ndi mtima wanga wonse; ndiyankheni Inu Yehova, ndipo ndidzamvera zophunzitsa zanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:145
14 Mawu Ofanana  

Yehova, imvani pemphero langa, ndipo mfuu wanga ufikire Inu.


Ndinakufunani ndi mtima wanga wonse; ndisasokere kusiyana nao malamulo anu.


Ndinalumbira, ndipo ndinatsimikiza mtima, kuti ndidzasamalira maweruzo anu olungama.


Mundichokere ochita zoipa inu; kuti ndisunge malamulo a Mulungu wanga.


Potero ndidzasamalira malamulo anu chisamalire kunthawi za nthawi.


Ndinapemba pankhope panu ndi mtima wanga wonse: Mundichitire chifundo monga mwa mau anu.


Ndidzasamalira malemba anu: Musandisiye ndithu.


Khulupirirani pa Iye nyengo zonse, anthu inu, tsanulirani mitima yanu pamaso pake. Mulungu ndiye pothawirapo ife.


Kondwetsani moyo wa mtumiki wanu; pakuti ndikwezera moyo wanga kwa Inu, Ambuye.


Ndipo mudzandifuna Ine, ndi kundipeza, pamene mundifuna ndi mtima wanu wonse.


Ndipo mkaziyo anali ndi mtima wowawa, napemphera kwa Yehova, naliratu misozi;


Ndipo Hana anayankha, nati, Iai, mbuyanga. Ine ndili mkazi wa mtima wachisoni; sindinamwe vinyo kapena chakumwa chowawa, koma ndinatsanulira mtima wanga pamaso pa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa