Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:14 - Buku Lopatulika

14 Ndinakondwera m'njira ya mboni zanu, koposa ndi chuma chonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ndinakondwera m'njira ya mboni zanu, koposa ndi chuma chonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Kuyenda m'njira ya malamulo anu kumandikondwetsa, kupambana kukhala ndi chuma chilichonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Ndimakondwera potsatira malamulo anu monga momwe munthu amakondwera akakhala ndi chuma chambiri.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:14
12 Mawu Ofanana  

Sindinabwerera kusiya malamulo a pa milomo yake; ndasungitsa mau a pakamwa pake koposa lamulo langalanga.


Aleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, wakukondwera kwambiri ndi malamulo ake.


Ndinalandira mboni zanu zikhale cholandira chosatha; pakuti ndizo zokondweretsa mtima wanga.


Chifukwa chake ndikonda malamulo anu koposa golide, inde golide woyengeka.


Ndikondwera nao mau anu, ngati munthu wakupeza zofunkha zambiri.


Ndipo ndidzadzikondweretsa nao malamulo anu, amene ndiwakonda.


Chilamulo cha pakamwa panu chindikomera koposa golide ndi siliva zikwizikwi.


Nsoni zokoma zanu zindidzere, kuti ndikhale ndi moyo; popeza chilamulo chanu chindikondweretsa.


Mau anu anapezeka, ndipo ndinawadya; mau anu anakhala kwa ine chikondwero ndi chisangalalo cha mtima wanga; pakuti ndatchedwa dzina lanu, Yehova Mulungu wa makamu.


Ufumu wa Kumwamba uli wofanana ndi chuma chobisika m'munda; chimene munthu anachipeza, nachibisa; ndipo m'kuchikonda kwake achoka, nagulitsa zonse ali nazo, nagula munda umenewu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa