Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:135 - Buku Lopatulika

135 Muwalitse nkhope yanu pa mtumiki wanu; ndipo mundiphunzitse malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

135 Muwalitse nkhope yanu pa mtumiki wanu; ndipo mundiphunzitse malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

135 Yang'anireni ine mtumiki wanu ndi chikondi chanu, ndipo mundiphunzitse malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

135 Nkhope yanu iwalire mtumiki wanu ndipo mundiphunzitse malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:135
14 Mawu Ofanana  

Apembedza Mulungu, ndipo amkomera mtima; m'mwemo aona nkhope yake mokondwera; ndipo ambwezera munthu chilungamo chake.


Chimene sindichiona mundilangize ndi Inu, ngati ndachita chosalungama sindidzabwerezanso.


wakutilangiza ife koposa nyama za padziko, wakutipatsa nzeru zoposa mbalame za m'mlengalenga?


Taonani, Mulungu achita mokwezeka mu mphamvu yake, mphunzitsi wakunga Iye ndani?


Inu ndinu wodala Yehova; ndiphunzitseni malemba anu.


Ndinafotokozera njira zanga, ndipo munandiyankha: Mundiphunzitse malemba anu.


Ambiri amati, Adzationetsa chabwino ndani? Weramutsirani ife kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.


Mbusa wa Israele, tcherani khutu; inu wakutsogolera Yosefe ngati nkhosa; inu wokhala pa akerubi, walitsani.


Mutibweze, Yehova Mulungu wa makamu; nimuwalitse nkhope yanu, ndipo tidzapulumuka.


Mutibweze, Mulungu; nimuwalitse nkhope yanu, ndipo tidzapulumuka.


Mulungu wa makamu, mutibweze; nimuwalitse nkhope yanu, ndipo tidzapulumuka.


Ndipo anawatsegulira mitima yao, kuti adziwitse malembo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa