Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:132 - Buku Lopatulika

132 Munditembenukire, ndi kundichitira chifundo, monga mumatero nao akukonda dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

132 Munditembenukire, ndi kundichitira chifundo, monga mumatero nao akukonda dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

132 Yang'aneni, ndipo mundikomere mtima monga m'mene mumachitira ndi anthu okukondani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

132 Tembenukirani kwa ine ndipo mundichitire chifundo, monga mumachitira nthawi zonse kwa iwo amene amakonda dzina lanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:132
10 Mawu Ofanana  

Kapena Yehova adzayang'anira chosayenerachi alikundichitira ine, ndipo Yehova adzandibwezera chabwino m'malo mwa kunditukwana kwa lero.


Mundikumbukire, Yehova, monga momwe muvomerezana ndi anthu anu; mundionetsa chipulumutso chanu:


Muchitire mtumiki wanu monga mwa chifundo chanu, ndipo ndiphunzitseni malemba anu.


Cheukirani ine ndipo ndichitireni chifundo; pakuti ndili wounguluma ndi wozunzika.


Penyani mazunzo anga ndi zovuta zanga; ndipo khululukirani zolakwa zanga zonse.


Pakuti Inu, Yehova, mudzadalitsa wolungamayo; mudzamtchinjiriza nacho chivomerezo ngati chikopa.


Ndipo anthuwo anakhulupirira; ndipo pamene anamva kuti Yehova adawazonda ana a Israele, ndi kuti adaona mazunzo ao, anawerama, nalambira Mulungu.


nalonjeza chowinda, nati, Yehova wa makamu, mukapenyera ndithu kusauka kwa mdzakazi wanu, ndi kukumbukira ine, ndi kusaiwala mdzakazi wanu, mukapatsa mdzakazi wanu mwana wamwamuna, ine ndidzampereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake, ndipo palibe lumo lidzapita pamutu pake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa