Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:128 - Buku Lopatulika

128 Chifukwa chake ndiyesa ngolunjika malangizo anu onse akunena zonse; koma ndidana nazo njira zonse zonyenga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

128 Chifukwa chake ndiyesa ngolunjika malangizo anu onse akunena zonse; koma ndidana nazo njira zonse zonyenga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

128 Malamulo anu onse amalungamitsa mayendedwe anga. Ndimadana ndi njira iliyonse yonyenga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

128 ndiponso chifukwa choti ndimaona kuti malangizo anu onse ndi wowongoka, ndimadana ndi njira iliyonse yoyipa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:128
13 Mawu Ofanana  

Apenyerera anthu, ndi kuti, ndinachimwa, ndaipsa choongokacho, ndipo sindinapindule nako.


Malangizo anu andizindikiritsa; chifukwa chake ndidana nao mayendedwe onse achinyengo.


Mupepula onse akusokera m'malemba anu; popeza chinyengo chao ndi bodza.


Lilime langa liimbire mau anu; pakuti malamulo anu onse ndiwo olungama.


Pamenepo sindidzachita manyazi, pakupenyerera malamulo anu onse.


Pakuti maweruzo ake onse anali pamaso panga, ndipo malemba ake sindinawachotse kwa ine.


Mau onse a Mulungu ali oyengeka; ndiye chikopa cha iwo amene amkhulupirira.


Chotero chilamulo chili choyera, ndi chilangizo chake nchoyera, ndi cholungama, ndi chabwino.


Pakuti tidziwa kuti chilamulo chili chauzimu; koma ine ndili wathupi, wogulitsidwa kapolo wa uchimo.


Koma ngati ndichita chimene sindichifuna, ndivomerezana nacho chilamulo kuti chili chabwino.


Pakuti monga mwa munthu wa m'kati mwanga, ine ndikondwera ndi chilamulo cha Mulungu:


Ndipo mtundu waukulu wa anthu ndi uti, wakukhala nao malemba ndi maweruzo olungama, akunga chilamulo ichi chonse ndichiika pamaso panu lero lino?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa