Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:114 - Buku Lopatulika

114 Inu ndinu pobisalapo panga, ndi chikopa changa; ndiyembekezera mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

114 Inu ndinu pobisalapo panga, ndi chikopa changa; ndiyembekezera mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

114 Inu ndinu malo anga obisalako ndiponso chishango changa, ndimakhulupirira mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

114 Inu ndinu pothawirapo panga ndi chishango changa; chiyembekezo changa chili mʼmawu anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:114
10 Mawu Ofanana  

Ndipo musandichotsere ndithu mau a choonadi pakamwa panga; pakuti ndinayembekeza maweruzo anu.


Iwo amene akuopani adzandiona ine nadzakondwera; popeza ndayembekezera mau anu.


Moyo wanga unakomoka ndi kukhumba chipulumutso chanu: Ndinayembekezera mau anu.


Ndipo Inu Yehova, ndinu chikopa changa; ulemerero wanga, ndi wondiweramutsa mutu wanga.


Ndifuula kwa Yehova ndi mau anga, ndipo andiyankha m'phiri lake loyera.


Inu ndinu mobisalira mwanga; m'nsautso mudzandisunga; mudzandizinga ndi nyimbo za chipulumutso.


Pakuti Yehova Mulungu ndiye dzuwa ndi chikopa; Yehova adzapatsa chifundo ndi ulemerero; sadzakaniza chokoma iwo akuyenda angwiro.


Ndipo munthu adzakhala monga pobisalira mphepo, ndi pousira chimphepo; monga mitsinje yamadzi m'malo ouma, monga mthunzi wa thanthwe lalikulu m'dziko lotopetsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa