Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:110 - Buku Lopatulika

110 Oipa ananditchera msampha; koma sindinasokere m'malangizo anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

110 Oipa ananditchera msampha; koma sindinasokera m'malangizo anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

110 Anthu oipa anditchera msampha, komabe sindisokera kuchoka m'njira ya malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

110 Anthu oyipa anditchera msampha, koma sindinasochere kuchoka pa malangizo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:110
16 Mawu Ofanana  

Ndinakufunani ndi mtima wanga wonse; ndisasokere kusiyana nao malamulo anu.


Munadzudzula odzikuza otembereredwa, iwo akusokera kusiyana nao malamulo anu.


Odzikuza anandinyoza kwambiri: koma sindinapatukanso nacho chilamulo chanu.


Odzikuza anandikumbira mbuna, ndiwo osasamalira chilamulo chanu.


Akadandithera padziko lapansi; koma ine sindinasiye malangizo anu.


Oipa anandilalira kundiononga; koma ndizindikira mboni zanu.


Odzikuza ananditchera msampha, nandibisira zingwe; anatcha ukonde m'mphepete mwa njira; ananditchera makwekwe.


Mundisunge ndisagwe mumsampha ananditcherawo, ndisakodwe m'makwekwe a iwo ochita zopanda pake.


Koma ine, monga gonthi, sindimva; ndipo monga munthu wosalankhula, sinditsegula pakamwa panga.


Mtima wanga wakhazikika, Mulungu, ndakhazika mtima; ndidzaimba, inde, ndidzaimba zolemekeza.


Mfuu umvekedwe m'nyumba zao, pamene muwatengera khamu la nkhondo dzidzidzi; pakuti akumba dzenje lakundigwira ine, anabisira mapazi anga misampha.


Ndipo podziwa Daniele kuti adatsimikiza cholembedwacho, analowa m'nyumba mwake, m'chipinda mwake, chimene mazenera ake anatseguka oloza ku Yerusalemu; ndipo anagwada maondo ake tsiku limodzi katatu, napemphera, navomereza pamaso pa Mulungu wake monga umo amachitira kale lonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa