Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:105 - Buku Lopatulika

105 Mau anu ndiwo nyali ya ku mapazi anga, ndi kuunika kwa panjira panga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

105 Mau anu ndiwo nyali ya ku mapazi anga, ndi kuunika kwa panjira panga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

105 mau anu ndiye nyale ya mapazi anga, ndipo amaunikira njira yanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

105 Mawu anu ndi nyale ya kumapazi kwanga ndi kuwunika kwa pa njira yanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:105
7 Mawu Ofanana  

muja nyali yake inawala pamutu panga, ndipo ndi kuunika kwake ndinayenda mumdima;


Pakuti Inu muyatsa nyali yanga; Yehova, Mulungu wanga, aunikira mdima wanga.


Malangizo a Yehova ali olungama, akukondweretsa mtima; malamulo a Yehova ali oyera, akupenyetsa maso.


Tumizirani kuunika kwanu ndi choonadi chanu zinditsogolere; zindifikitse kuphiri lanu loyera, kumene mukhala Inuko.


Pakuti malangizo ndi nyali, malamulo ndi kuunika; ndi zidzudzulo za mwambo ndizo njira ya moyo.


Koma zinthu zonse potsutsika ndi kuunika, zionekera; pakuti chonse chakuonetsa chili kuunika.


Ndipo tili nao mau a chinenero okhazikika koposa; amene muchita bwino powasamalira, monga nyali younikira m'malo a mdima, kufikira kukacha, nikauka nthanda pa mtima yanu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa