Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:100 - Buku Lopatulika

100 Ndizindikira koposa okalamba popeza ndinasunga malangizo anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

100 Ndizindikira koposa okalamba popeza ndinasunga malangizo anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

100 Ndili ndi nzeru kupambana okalamba, pakuti ndimatsata malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

100 Ndili ndi nzeru zochuluka zomvetsera zinthu kuposa anthu okalamba, popeza ndimamvera malangizo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:100
11 Mawu Ofanana  

Kwa okalamba kuli nzeru, ndi kwa a masiku ochuluka luntha.


Koma kwa munthu anati, Taonani, kuopa Ambuye ndiko nzeru; ndi kupatukana nacho choipa ndiko luntha.


Ndipo Elihu analindira kulankhula ndi Yobu, popeza akulu misinkhu ndi iwowa.


Kumuopa Yehova ndiko chiyambi cha nzeru; onse akuchita chotero ali nacho chidziwitso chokoma; chilemekezo chake chikhalitsa kosatha.


Mundizindikiritse, ndipo ndidzasunga malamulo anu; ndidzawasamalira ndi mtima wanga wonse.


Chifukwa chimenechi yense amene akamva mau anga amenewa, ndi kuwachita, ndidzamfanizira iye ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe;


Ndani ali wanzeru, ndi waluso mwa inu? Aonetsere ndi mayendedwe ake abwino ntchito zake mu nzeru yofatsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa