Masalimo 116:9 - Buku Lopatulika9 Ndidzayenda pamaso pa Yehova m'dziko la amoyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndidzayenda pamaso pa Yehova m'dziko la amoyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndimayenda pamaso pa Chauta m'dziko la amoyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 kuti ine ndiyende pamaso pa Yehova mʼdziko la anthu amoyo. Onani mutuwo |