Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 116:8 - Buku Lopatulika

8 Pakuti munalanditsa moyo wanga kuimfa, maso anga kumisozi, mapazi anga, ndingagwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Pakuti munalanditsa moyo wanga kuimfa, maso anga kumisozi, mapazi anga, ndingagwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Pakuti Inu Chauta, mwandipulumutsa ku imfa, mwaletsa misozi yanga, mwanditeteza kuti ndisaphunthwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Pakuti Inu Yehova mwapulumutsa moyo wanga ku imfa, maso anga ku misozi, mapazi anga kuti angapunthwe,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 116:8
10 Mawu Ofanana  

Angakhale akagwa, satayikiratu, pakuti Yehova agwira dzanja lake.


Koma Mulungu adzaombola moyo wanga kumphamvu ya manda. Pakuti adzandilandira ine.


Pakuti mwalanditsa moyo wanga kuimfa, simunatero nao mapazi anga kuti ndingagwe? Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu m'kuunika kwa amoyo.


Pakuti chifundo chanu cha pa ine nchachikulu; ndipo munalanditsa moyo wanga kunsi kwa manda.


Pamene ndinati, Literereka phazi langa, chifundo chanu, Yehova, chinandichirikiza.


Iye wameza imfa kunthawi yonse; ndipo Ambuye Mulungu adzapukuta misozi pa nkhope zonse; ndipo chitonzo cha anthu ake adzachichotsa padziko lonse lapansi; chifukwa Yehova wanena.


Ukanene kwa Hezekiya, Atero Yehova, Mulungu wa Davide, kholo lako, Ndamva kupemphera kwako, ndaona misozi yako; taona, ndidzaonjezera pa masiku ako zaka khumi ndi zisanu.


ndipo adzawapukutira misozi yonse kuichotsa pamaso pao; ndipo sipadzakhalanso imfa; ndipo sipadzakhalanso maliro, kapena kulira, kapena chowawitsa; zoyambazo zapita.


chifukwa Mwanawankhosa wakukhala pakati pa mpando wachifumu adzawaweta, nadzawatsogolera ku akasupe a madzi amoyo, ndipo Mulungu adzawapukutira misozi yonse pamaso pao.


Ndipo alonda anaona munthu alikutuluka m'mzinda, nanena naye, Utionetsetu polowera m'mzinda, ndipo tidzakuchitira chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa