Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 116:7 - Buku Lopatulika

7 Ubwere moyo wanga ku mpumulo wako; pakuti Yehova anakuchitira chokoma.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ubwere moyo wanga ku mpumulo wako; pakuti Yehova anakuchitira chokoma.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Iwe mtima wanga, bwerera ku malo ako opumulira, chifukwa Chauta wakuchitira zokoma.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Pumula iwe moyo wanga, pakuti Yehova wakuchitira zokoma.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 116:7
8 Mawu Ofanana  

Muchitire chokoma mtumiki wanu kuti ndikhale ndi moyo; ndipo ndidzasamalira mau anu.


Ndidzaimbira Yehova, pakuti anandichitira zokoma.


Chifukwa chake ndinalumbira mu mkwiyo wanga, ngati adzalowa mpumulo wanga.


Ndipo usaope, iwe Yakobo mtumiki wanga, ati Yehova; usaope, iwe Israele; pakuti, taona, ndidzakupulumutsa iwe kutali, ndi mbeu zako kudziko la undende wao; ndipo Yakobo adzabwera, nadzakhala ndi mtendere, ndipo adzakhala chete, palibe amene adzamuopsa.


Yehova atero, Imani m'njira ndi kuona, funsani za mayendedwe akale, m'menemo muli njira yabwino, muyende m'menemo, ndipo mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu; koma anati, Sitidzayendamo.


Ndipo adzatsata omkonda koma osawagwira, adzawafunafuna koma osawapeza; pamenepo adzati, Ndidzamuka ndi kubwererana ndi mwamuna wanga woyamba, popeza pamenepo panandikomera koposa tsopano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa