Masalimo 116:18 - Buku Lopatulika18 Ndidzachita zowinda zanga za kwa Yehova, tsopano, pamaso pa anthu ake onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndidzachita zowinda zanga za kwa Yehova, tsopano, pamaso pa anthu ake onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndidzachita zimene ndidalumbira kwa Chauta pamaso pa anthu ake onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndidzakwaniritsa malonjezo anga kwa Yehova pamaso pa anthu ake onse, Onani mutuwo |