Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 116:12 - Buku Lopatulika

12 Ndidzabwezera Yehova chiyani chifukwa cha zokoma zake zonse anandichitira?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndidzabwezera Yehova chiyani chifukwa cha zokoma zake zonse anandichitira?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ndidzambwezera chiyani Chauta pa zabwino zonse zimene adandichitira?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ndingamubwezere chiyani Yehova, chifukwa cha zokoma zake zonse zimene wandichitira?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 116:12
8 Mawu Ofanana  

Koma Hezekiya sanabwezere monga mwa chokoma anamchitira, pakuti mtima wake unakwezeka; chifukwa chake unamdzera mkwiyo iye, ndi Yuda, ndi Yerusalemu.


Lemekeza Yehova, moyo wanga, ndi kusaiwala zokoma zake zonse atichitirazi:


Ndidzafika kwa Yehova ndi chinai, ndi kuwerama kwa Mulungu Wam'mwamba? Kodi ndifike kwa Iye ndi nsembe zopsereza, ndi anaang'ombe a chaka chimodzi?


Chifukwa chake ndikupemphani inu, abale, mwa zifundo za Mulungu, kuti mupereke matupi anu nsembe yamoyo, yopatulika, yokondweretsa Mulungu, ndiko kupembedza kwanu koyenera.


Pakuti munagulidwa ndi mtengo wake wapatali; chifukwa chake lemekezani Mulungu m'thupi lanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa