Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 116:11 - Buku Lopatulika

11 Pofulumizidwa mtima ndinati ine, anthu onse nga mabodza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Pofulumizidwa mtima ndinati ine, anthu onse nga mabodza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Pamene ndinkachita mantha, ndidati, “Anthu ndi osakhulupirika.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ndipo ndili mʼnkhawa yanga ndinati, “Anthu onse ndi abodza.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 116:11
8 Mawu Ofanana  

Ndipo anati, Nyengo ino chaka chikudzachi udzafukata mwana wamwamuna. Koma anati, Iai, mbuyanga, munthu wa Mulungu, musanamiza mdzakazi wanu.


Amanena za bodza munthu yense ndi mnansi wake, amanena ndi mlomo wothyasika, ndi mitima iwiri.


Yehova adzadula milomo yonse yothyasika, lilime lakudzitamandira;


Ndipo ine, pakutenga nkhawa, ndinati, Ndadulidwa kundichotsa pamaso panu. Komatu munamva mau a kupemba kwanga pamene ndinafuulira kwa Inu.


Indetu, anthu achabe ndi mpweya, ndipo anthu aakulu ndi bodza, pakuwayesa apepuka; onse pamodzi apepuka koposa mpweya.


Msatero ai. Koma Mulungu akhale woona, ndipo anthu onse akhale onama; monga kwalembedwa, Kuti Inu mukayesedwe wolungama m'maneno anu, ndi kuti mukapambane m'mene muweruzidwa.


Ndipo Davide ananena mumtima mwake, Tsiku lina Saulo adzandipha; palibe china chondikomera koma kuti ndithawire ku dziko la Afilisti; ndipo Saulo adzakhala kakasi chifukwa cha ine, osandifunanso m'malire onse a Israele, momwemo ndidzapulumuka m'dzanja lake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa