Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 115:18 - Buku Lopatulika

18 Koma ife tidzalemekeza Yehova kuyambira tsopano kufikira nthawi yonse. Aleluya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Koma ife tidzalemekeza Yehova kuyambira tsopano kufikira nthawi yonse. Aleluya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Koma ife tidzatamanda Chauta kuyambira tsopano mpaka muyaya. Tamandani Chauta!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 ndi ife amene timatamanda Yehova, kuyambira tsopano mpaka muyaya. Tamandani Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 115:18
6 Mawu Ofanana  

Lodala dzina la Yehova Kuyambira tsopano kufikira kosatha.


Masiku onse ndidzakuyamikani; ndi kulemekeza dzina lanu kunthawi za nthawi.


Pakamwa panga padzanena chilemekezo cha Yehova; ndi zinthu zonse zilemekeze dzina lake loyera kunthawi za nthawi.


Daniele anayankha, nati, Lilemekezedwe dzina la Mulungu kunthawi za nthawi, pakuti nzeru ndi mphamvu zili zake;


Ndipo cholengedwa chilichonse chili m'mwamba, ndi padziko, ndi pansi padziko, ndi m'nyanja, ndi zonse zili momwemo, ndinazimva zilikunena, Kwa Iye wakukhala pa mpando wachifumu, ndi kwa Mwanawankhosa zikhale chiyamiko, ndi ulemu, ndi ulemerero, ndi mphamvu, kufikira nthawi za nthawi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa